Chidule cha 1 Atesalonika
I. Moni 1:1
II. Pemphero lachiyamiko 1:2-4
III. Utumiki wa Paulo pa Atesalonika 1:5-2:16
A. Kulandiridwa kwa Uthenga Wabwino 1:5-10
B. Khalidwe la utumiki wa Paulo 2:1-16
IV. Ubale wa Paulo ndi Atesalonika 2:17-3:13
A. Kufuna kwa Paulo kubwerera 2:17-18
B. Chisangalalo cha Paulo mu Atesalonika 2:19-20
C. Ntchito ya Timoteo 3:1-5
D. Lipoti la Timoteo 3:6-7
E. Kukhutitsidwa kwa Paulo 3:8-12
F. Pemphero la Paulo 3:11-13
V. Langizo la Paulo ku moyo wachikhristu 4:1-12
A. Malangizo onse 4:1-2
B. Chiyero pa kugonana 4:3-8
C. Chikondi cha pa abale 4:9-10
D. Kupeza moyo 4:11-12
VI. Malangizo a Paulo pa kudza kwachiwiri 4:13-5:11
A. Anthu 4:13-18
B. Nthawi 5:1-3
C. Chotsutsa 5:4-11
VII. Mlandu womaliza wa Paulo 5:12-22
VIII. Kumaliza 5:23-28